• Home
  • The Mission
    • About us
    • Prayer & Praise Updates
    • Priority Projects
    • Boxes with Love
    • Prayer Articles
    • Prayer Maps
    • Projects
    • Literature4Africa
    • Missionary Reports
    • Hammond Family News
    • In Memorium
  • Video & Audio Gallery
    • Audio Gallery
    • Video Gallery
  • Newsletters
  • Resources
    • Digital Resources
    • Articles >
      • Articles
      • News
      • Africa
      • Animals
      • Animism
      • Bible Teaching
      • Christmas
      • Family
      • Gun Control & Self Defense
      • History
      • Islam
      • Missions
      • Persecution
      • Political & Social Issues
      • War and Terrorism
    • Film Reviews
    • Bible Studies
    • Answers to Critical Questions
    • Skeptics Questions Answered
    • Articles in other Languages >
      • Afrikaans
      • German
      • French
      • Danish
      • Chinese
      • Russian
      • Chichewa
      • Czech
    • Links
    • Resource Posters
    • Books published by Dr Peter Hammond
  • Events
  • Contact Us
  • Donate
Frontline Fellowship
  • Home
  • The Mission
    • About us
    • Prayer & Praise Updates
    • Priority Projects
    • Boxes with Love
    • Prayer Articles
    • Prayer Maps
    • Projects
    • Literature4Africa
    • Missionary Reports
    • Hammond Family News
    • In Memorium
  • Video & Audio Gallery
    • Audio Gallery
    • Video Gallery
  • Newsletters
  • Resources
    • Digital Resources
    • Articles >
      • Articles
      • News
      • Africa
      • Animals
      • Animism
      • Bible Teaching
      • Christmas
      • Family
      • Gun Control & Self Defense
      • History
      • Islam
      • Missions
      • Persecution
      • Political & Social Issues
      • War and Terrorism
    • Film Reviews
    • Bible Studies
    • Answers to Critical Questions
    • Skeptics Questions Answered
    • Articles in other Languages >
      • Afrikaans
      • German
      • French
      • Danish
      • Chinese
      • Russian
      • Chichewa
      • Czech
    • Links
    • Resource Posters
    • Books published by Dr Peter Hammond
  • Events
  • Contact Us
  • Donate

Chikristu ndi Chislamu

17/10/2017

0 Comments

 
​Pakuti mtundu ndi ufumu umene udzakana kutumikira udzaonongeka, inde mitundu imeneyo idzasakazidwa ndithu" Yesaya 60:12. Paciyam, bi Mulungu adalenga kumwamba ndi dziko lapansi Genesis 1:1 ndipo anati Mulungu, Tipange munthu m' chifanizo chathu. Monga mwa chikhalidwe chathu: Genesis 1:26 Lero pa dziko lonse lapansi maiko ambiri adalandira ufulu odzilamurila, komankhondo imene yasautsa anthu ambiri ndi kudziwa Mulungu woona amene ayenela kumukhulupirila ndi kumulambira. Mulungu wolenga kumwamba ndi dziko lapansi anati “usakhale nayo milungu ina koma ine ndekha"
Eksodo 20:3.
CHISALAMU

Chislamu ndi chipembedzo chokhala ndi m'tsogoleri wake, malamulo ake ndi miyambo yakenso. M'tsogoleri wa Chislamu ndi munthu amene adamwalira dzina lake Muhammod . Muhammod anabadwa m'chaka cha 570 AD, anayamba nchito yake monga m'neneri m'chaka cha 613 AD, ndipo anamwalira mchaka cha 632 AD. Chisalamu chili ndi mizati imnene chiyadzamilapo. Olemba buku lochedwa "Understanding Islam" anati mizatiyi ilipo isanu, koma olemba "Slavery, Terrorism and Islam" Dr. Peter Hammond anati Pali mizatu isanu ndi umodzi (6) nati anthuwa anati mizati ya chipembezo chawo ndi 5, chifukwa wa 6 ndi nkhondo imene anaicha "nkhondo yoyera" Jihad.
 
Koma inayi ndi iyi:
 
1. Shahada - Kuvomereza poyera chikhulupiriro chawo.
2. Sawn - Kusala kudya mwezi wa Ramadan onse, atadya madzulo, mpaka m'wama.
3. Salah - Kupemphera kasanu pa tsiku limodzi.
4. Zakah - Kupatsa chaufulu kwa ena (koma molengeza).
5.Hajj - Ulendo wa ku Mecca ngakhale kamodzi mu umoyo onse.
Ma muslimu amakhulupirira pa zinthu 5 kuti avomerezeke kukhala m'modzi wa iwo.
 
1.Mulungu umodzi (allah).
2.Angelo alipodi.
3.Mabuku onse ovumbulutsidwa asanu olembedwa ndi Moses, Salimo la David, chipangano chatsopano ndi Quran.
4.Aneneri otumidwa ndi Mulungu pakati pawo pali Muhammod ndi Yesu.
5.Kuuka kwa a kufa, kumene kuphatikiza ulosi wa Tsiku Lomariza la chiweruzo kumene adzaonetsa kopita, m'silamu, ku Gehena kapena ku paradiso.
 
CHIKHRISTU

Chikristu ndi moyo umene umapezeka mwa m'tsogoleri amene anati ine ndine kuuka ndi moyo yense okhulupirira ine angakhale amwalira adzakhala ndi moyo" Yohane 11:25 - 26.

Zipembedzo zili ndi kumene zalinga, zili paulendo opita kumapeto, ulendo ulionse uli ndi njira yake. Mtsogoreli wa Chikristu Yesu anati: mapeto a Chikristu ndi moyo wosatha, ndipo kuti munthu akafike ku moyo wosatha, mjira yake ndi Yohane 14:6. Chikristu si chipembedzo chabe koma moyo. Akristu Buku lawo ndi Baibulo mau ake a Mulungu . Asilamu Buku lawo ndi Quran imene anati Muhammod adalandila kwa m'ngelo Gabriel.

Quran - Baibulo

Buku limodzi - Mabuku 66

Wolemba mnthu umodzi - Wolemba anthu 40

Chilankhulidwe chimodzi - Zilankhulo 3

Dziko limodzi - Makontinenti 3

Lolembedwa mu zaka23 - Lombedwa mu zaka 1500

Mulibe Ulosi - Muli Ulosi

Mulibe Zodabwitsa - Muli Zodabwitsa

Manda ku Medina - Manda apululu ku Yerusalemu

Mulibe Chiwombolo - Muli Chiwombolo

Muli adani pa adani - Chikondi pa adani

Muli ukapapolo - Muli Ufulu

Pamene mukuwerenga pepala iyi, dziwani kuti mwapatsidwa mwayi osankha chimene muyenela kutsatira, chifukwa tsiku lina mwayi umenewu udzakhala utakutherani. Mudzaufuna koma sudzapezeka. Lero ngati inu mukhulupirira Ambuye Yesu mudzapulumuka. Machitidwe 16:31 pakuti palibe dzina lina limene tingapulumutsidwe nalo Machitidwe 4:12 kuti mudziwe zambiri, kapena muli ndi funso lembelani ku keyala iyi.
0 Comments



Leave a Reply.

    More Articles

    All
    CHIKRISTU NDI CHISLAMU

    Archives

    October 2017

    RSS Feed

"And Jesus came and spoke to them, saying, “All authority has been given to Me in heaven and on earth. 
Go therefore and make disciples of all the nations, baptizing them in the name of the Father and of the Son and of the Holy Spirit, 
teaching them to observe all things that I have commanded you; and lo, I am with you always, even to the end of the age.” Amen.
.”
 Matthew 28: 18-20
Picture

P.O.Box 74 Newlands 7725
Cape Town South Africa

Tel:  +27 (0)21 689 4480 
Email: admin@frontline.org.za
  • Home
  • The Mission
    • About us
    • Prayer & Praise Updates
    • Priority Projects
    • Boxes with Love
    • Prayer Articles
    • Prayer Maps
    • Projects
    • Literature4Africa
    • Missionary Reports
    • Hammond Family News
    • In Memorium
  • Video & Audio Gallery
    • Audio Gallery
    • Video Gallery
  • Newsletters
  • Resources
    • Digital Resources
    • Articles >
      • Articles
      • News
      • Africa
      • Animals
      • Animism
      • Bible Teaching
      • Christmas
      • Family
      • Gun Control & Self Defense
      • History
      • Islam
      • Missions
      • Persecution
      • Political & Social Issues
      • War and Terrorism
    • Film Reviews
    • Bible Studies
    • Answers to Critical Questions
    • Skeptics Questions Answered
    • Articles in other Languages >
      • Afrikaans
      • German
      • French
      • Danish
      • Chinese
      • Russian
      • Chichewa
      • Czech
    • Links
    • Resource Posters
    • Books published by Dr Peter Hammond
  • Events
  • Contact Us
  • Donate